2 Samueli 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Husai+ mbadwa ya Areki,+ mnzake wa Davide, atafika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!” 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2017, tsa. 29
16 Husai+ mbadwa ya Areki,+ mnzake wa Davide, atafika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”