-
2 Samueli 16:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Zitatero Abisalomu anafunsa Husai kuti: “Kodi zimene wachitazi wamusonyeza mnzako chikondi chokhulupirika? Nʼchifukwa chiyani sunapite naye limodzi mnzakoyo?”
-