2 Samueli 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndibwereze kunena kuti, ndingatumikirenso ndani? Ndiyenera kutumikira mwana wake. Ine ndikutumikirani inuyo ngati mmene ndinkachitira ndi bambo anu.”+
19 Ndibwereze kunena kuti, ndingatumikirenso ndani? Ndiyenera kutumikira mwana wake. Ine ndikutumikirani inuyo ngati mmene ndinkachitira ndi bambo anu.”+