2 Samueli 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ugone ndi akazi aangʼono* a bambo ako+ amene awasiya kuti azisamalira nyumba.*+ Ukatero Aisiraeli onse adzamva kuti wadzinunkhitsa pamaso pa bambo ako, ndipo udzapatsa mphamvu anthu amene ali kumbali yako.” 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:21 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 13
21 Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ugone ndi akazi aangʼono* a bambo ako+ amene awasiya kuti azisamalira nyumba.*+ Ukatero Aisiraeli onse adzamva kuti wadzinunkhitsa pamaso pa bambo ako, ndipo udzapatsa mphamvu anthu amene ali kumbali yako.”