2 Samueli 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho anamangira Abisalomu tenti padenga,+ ndipo Abisalomu anayamba kugona ndi akazi aangʼono a bambo ake,+ Aisiraeli onse akuona.+
22 Choncho anamangira Abisalomu tenti padenga,+ ndipo Abisalomu anayamba kugona ndi akazi aangʼono a bambo ake,+ Aisiraeli onse akuona.+