2 Samueli 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikamupeza atatopa komanso alibe mphamvu*+ ndipo ndikamupanikiza. Zikakatero, anthu onse amene ali naye akathawa ndipo ine ndikapha mfumu yokhayo.+
2 Ndikamupeza atatopa komanso alibe mphamvu*+ ndipo ndikamupanikiza. Zikakatero, anthu onse amene ali naye akathawa ndipo ine ndikapha mfumu yokhayo.+