2 Samueli 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Husai anauza Abisalomu kuti: “Malangizo amene Ahitofeli wapereka ulendo uno, si abwino.”+