2 Samueli 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zikatero, ngakhale mwamuna wolimba mtima ngati mkango+ adzachita mantha kwambiri. Chifukwa Aisiraeli onse akudziwa kuti bambo anu ndi munthu wamphamvu+ ndipo amuna amene ali nawo ndi olimba mtima. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:10 Nsanja ya Olonda,7/15/1996, tsa. 32
10 Zikatero, ngakhale mwamuna wolimba mtima ngati mkango+ adzachita mantha kwambiri. Chifukwa Aisiraeli onse akudziwa kuti bambo anu ndi munthu wamphamvu+ ndipo amuna amene ali nawo ndi olimba mtima.