2 Samueli 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Malangizo anga ndi akuti: Musonkhanitse Aisiraeli onse kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba.+ Akhale ambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja+ ndipo inuyo muwatsogolere kunkhondo.
11 Malangizo anga ndi akuti: Musonkhanitse Aisiraeli onse kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba.+ Akhale ambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja+ ndipo inuyo muwatsogolere kunkhondo.