2 Samueli 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Husai anauza Zadoki ndi Abiyatara+ ansembe kuti: “Ahitofeli wapereka malangizo akutiakuti kwa Abisalomu ndi akulu a Isiraeli koma ine ndapereka malangizo akutiakuti.
15 Kenako Husai anauza Zadoki ndi Abiyatara+ ansembe kuti: “Ahitofeli wapereka malangizo akutiakuti kwa Abisalomu ndi akulu a Isiraeli koma ine ndapereka malangizo akutiakuti.