2 Samueli 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiye tumizani uthenga mwamsanga kwa Davide wakuti, ‘Usiku uno musakhale pamalo owolokera kuchipululu. Koma muwoloke ndithu chifukwa mukapanda kutero inu mfumu ndi anthu onse amene muli nawo, muphedwa.’”+
16 Ndiye tumizani uthenga mwamsanga kwa Davide wakuti, ‘Usiku uno musakhale pamalo owolokera kuchipululu. Koma muwoloke ndithu chifukwa mukapanda kutero inu mfumu ndi anthu onse amene muli nawo, muphedwa.’”+