2 Samueli 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yonatani+ ndi Ahimazi+ ankakhala ku Eni-rogeli+ ndipo wantchito wamkazi anapita kukawauza uthengawu. Choncho iwo ananyamuka kuti akauze Mfumu Davide. Iwo sanafune kuti anthu awaone akulowa mumzinda. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:17 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 20-21
17 Yonatani+ ndi Ahimazi+ ankakhala ku Eni-rogeli+ ndipo wantchito wamkazi anapita kukawauza uthengawu. Choncho iwo ananyamuka kuti akauze Mfumu Davide. Iwo sanafune kuti anthu awaone akulowa mumzinda.