2 Samueli 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komabe mnyamata wina anawaona ndipo anapita kukauza Abisalomu. Choncho anthu awiriwo anachoka mofulumira nʼkupita kunyumba kwa munthu wina amene anali ndi chitsime pakhomo pake ku Bahurimu,+ ndipo analowa mʼchitsimemo.
18 Komabe mnyamata wina anawaona ndipo anapita kukauza Abisalomu. Choncho anthu awiriwo anachoka mofulumira nʼkupita kunyumba kwa munthu wina amene anali ndi chitsime pakhomo pake ku Bahurimu,+ ndipo analowa mʼchitsimemo.