-
2 Samueli 17:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Nthawi yomweyo Davide ananyamuka pamodzi ndi anthu onse amene anali naye, ndipo anawoloka Yorodano. Pofika mʼbandakucha, aliyense anali atawoloka Yorodano.
-