25 Ndiyeno Abisalomu anasankha Amasa+ kukhala mtsogoleri wa asilikali mʼmalo mwa Yowabu.+ Amasa anali mwana wa munthu wina wa Chiisiraeli dzina lake Itara yemwe anagona ndi Abigayeli+ mwana wamkazi wa Nahasi, mchemwali wake wa Zeruya, mayi ake a Yowabu.