2 Samueli 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Davide atangofika ku Mahanaimu, Sobi mwana wamwamuna wa Nahasi wochokera ku Raba+ mzinda wa Aamoni, Makiri+ mwana wa Amiyeli wochokera ku Lo-debara komanso Barizilai+ wa ku Giliyadi wochokera ku Rogelimu,
27 Davide atangofika ku Mahanaimu, Sobi mwana wamwamuna wa Nahasi wochokera ku Raba+ mzinda wa Aamoni, Makiri+ mwana wa Amiyeli wochokera ku Lo-debara komanso Barizilai+ wa ku Giliyadi wochokera ku Rogelimu,