2 Samueli 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 uchi, nkhosa, bata ndiponso tchizi.* Anabweretsa zinthu zimenezi kuti Davide ndi anthu onse amene anali naye adye.+ Iwo ankati: “Anthuwa ali mʼchipululu ndipo ali ndi njala, ali ndi ludzu komanso atopa.”+
29 uchi, nkhosa, bata ndiponso tchizi.* Anabweretsa zinthu zimenezi kuti Davide ndi anthu onse amene anali naye adye.+ Iwo ankati: “Anthuwa ali mʼchipululu ndipo ali ndi njala, ali ndi ludzu komanso atopa.”+