-
2 Samueli 18:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mfumu inawauza kuti: “Ndichita zilizonse zimene inu mukuona kuti nʼzabwino.” Choncho mfumu inaima pafupi ndi geti ndipo anthu onsewo anapita kunkhondo mʼmagulu a anthu 100 ndi 1,000.
-