2 Samueli 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu inalamula Yowabu, Abisai ndi Itai kuti: “Musakachitire nkhanza Abisalomu chifukwa mwana ameneyu ndimamukonda.”+ Anthu onse anamva zimene mfumu inalamula atsogoleriwa zokhudza Abisalomu.
5 Ndiyeno mfumu inalamula Yowabu, Abisai ndi Itai kuti: “Musakachitire nkhanza Abisalomu chifukwa mwana ameneyu ndimamukonda.”+ Anthu onse anamva zimene mfumu inalamula atsogoleriwa zokhudza Abisalomu.