2 Samueli 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Yowabu anati: “Usandichedwetse iwe!” Atatero anatenga zobayira* zitatu ndipo anakabaya Abisalomu pamtima ali moyo pakati pa ziyangoyango za mtengo waukulu.
14 Koma Yowabu anati: “Usandichedwetse iwe!” Atatero anatenga zobayira* zitatu ndipo anakabaya Abisalomu pamtima ali moyo pakati pa ziyangoyango za mtengo waukulu.