2 Samueli 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Atatero, anatenga Abisalomu nʼkumuponya mʼdzenje lalikulu mʼnkhalangomo ndipo anaunjikapo mulu waukulu kwambiri wa miyala.+ Koma Aisiraeli onse anathawa nʼkupita kunyumba kwawo.
17 Atatero, anatenga Abisalomu nʼkumuponya mʼdzenje lalikulu mʼnkhalangomo ndipo anaunjikapo mulu waukulu kwambiri wa miyala.+ Koma Aisiraeli onse anathawa nʼkupita kunyumba kwawo.