2 Samueli 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Davide anali atakhala pakati pa mageti awiri a mzinda+ ndipo mlonda+ anakwera padenga la geti lolumikizana ndi mpanda. Ndiyeno anaona munthu akuthamanga ali yekha.
24 Davide anali atakhala pakati pa mageti awiri a mzinda+ ndipo mlonda+ anakwera padenga la geti lolumikizana ndi mpanda. Ndiyeno anaona munthu akuthamanga ali yekha.