2 Samueli 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mlondayo anati: “Mmene munthu woyambayo akuthamangira, ndikuona ngati ndi Ahimazi+ mwana wa Zadoki.” Atatero, mfumu inati: “Ahimazi ndi munthu wabwino, ndipo amabwera ndi uthenga wabwino.”
27 Mlondayo anati: “Mmene munthu woyambayo akuthamangira, ndikuona ngati ndi Ahimazi+ mwana wa Zadoki.” Atatero, mfumu inati: “Ahimazi ndi munthu wabwino, ndipo amabwera ndi uthenga wabwino.”