-
2 Samueli 19:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Choncho pa tsikuli anthu onse anali pa chisoni mʼmalo mosangalala kuti apambana kunkhondo chifukwa anamva kuti: “Mfumu ikulira maliro a mwana wake.”
-