2 Samueli 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu a mʼmafuko onse a Isiraeli anayamba kukangana ndipo ankati: “Mfumuyi ndi imene inatipulumutsa kwa adani athu+ komanso kwa Afilisiti. Koma panopa yathawa mʼdziko lino chifukwa cha Abisalomu.+
9 Anthu a mʼmafuko onse a Isiraeli anayamba kukangana ndipo ankati: “Mfumuyi ndi imene inatipulumutsa kwa adani athu+ komanso kwa Afilisiti. Koma panopa yathawa mʼdziko lino chifukwa cha Abisalomu.+