2 Samueli 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu Davide inatumiza uthenga kwa Zadoki+ ndi Abiyatara+ ansembe wakuti: “Muwafunse akulu a Yuda+ kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani inu nokha simukuchita chilichonse kuti mfumu ibwerere kunyumba yake, pamene Aisiraeli onse atumiza uthenga kwa mfumu?
11 Mfumu Davide inatumiza uthenga kwa Zadoki+ ndi Abiyatara+ ansembe wakuti: “Muwafunse akulu a Yuda+ kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani inu nokha simukuchita chilichonse kuti mfumu ibwerere kunyumba yake, pamene Aisiraeli onse atumiza uthenga kwa mfumu?