2 Samueli 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amasa mumuuze kuti,+ ‘Iwe ndi ine ndife magazi amodzi. Mulungu andilange mowirikiza ngati sindikuika kukhala mtsogoleri wa gulu langa lankhondo mʼmalo mwa Yowabu.’”+
13 Amasa mumuuze kuti,+ ‘Iwe ndi ine ndife magazi amodzi. Mulungu andilange mowirikiza ngati sindikuika kukhala mtsogoleri wa gulu langa lankhondo mʼmalo mwa Yowabu.’”+