2 Samueli 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno mfumu inayamba kubwerera kwawo ndipo inafika ku Yorodano. Anthu a ku Yuda anabwera ku Giligala+ kudzakumana ndi mfumu komanso kuti aiperekeze powoloka mtsinje wa Yorodano.
15 Ndiyeno mfumu inayamba kubwerera kwawo ndipo inafika ku Yorodano. Anthu a ku Yuda anabwera ku Giligala+ kudzakumana ndi mfumu komanso kuti aiperekeze powoloka mtsinje wa Yorodano.