2 Samueli 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Simeyi+ mwana wa Gera wa ku Bahurimu, wa fuko la Benjamini, anathamangira amuna a ku Yuda nʼkupita nawo kukakumana ndi Mfumu Davide.
16 Kenako Simeyi+ mwana wa Gera wa ku Bahurimu, wa fuko la Benjamini, anathamangira amuna a ku Yuda nʼkupita nawo kukakumana ndi Mfumu Davide.