2 Samueli 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anali ndi amuna 1,000 a ku Benjamini. Nayenso Ziba,+ mtumiki wa nyumba ya Sauli, ndi ana ake 15 komanso atumiki ake 20 anayenda mofulumira nʼkukafika ku Yorodano mfumu isanafike.
17 Iye anali ndi amuna 1,000 a ku Benjamini. Nayenso Ziba,+ mtumiki wa nyumba ya Sauli, ndi ana ake 15 komanso atumiki ake 20 anayenda mofulumira nʼkukafika ku Yorodano mfumu isanafike.