-
2 Samueli 19:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ine mtumiki wanu ndikudziwa kuti ndinachimwa, nʼchifukwa chake lero ndakhala woyamba mʼnyumba yonse ya Yosefe kubwera kuno kudzakumana nanu mbuyanga mfumu.”
-