2 Samueli 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nayenso Mefiboseti,+ mdzukulu wa Sauli, anabwera kudzaonana ndi mfumu. Kuchokera tsiku limene mfumu inachoka mpaka tsiku lomwe inabwerera mwamtendere, iye sanasambe mapazi ake, sanamete ndevu zapamulomo ndiponso sanachape zovala zake.
24 Nayenso Mefiboseti,+ mdzukulu wa Sauli, anabwera kudzaonana ndi mfumu. Kuchokera tsiku limene mfumu inachoka mpaka tsiku lomwe inabwerera mwamtendere, iye sanasambe mapazi ake, sanamete ndevu zapamulomo ndiponso sanachape zovala zake.