2 Samueli 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye anayankha kuti: “Mbuyanga mfumu, mtumiki wanga+ ndi amene anandipusitsa. Ine mtumiki wanu ndinamuuza kuti, ‘Ndiikireni chishalo pabulu ndikwerepo kuti ndipite limodzi ndi mfumu,’ chifukwa ine mtumiki wanu ndine wolumala.+
26 Iye anayankha kuti: “Mbuyanga mfumu, mtumiki wanga+ ndi amene anandipusitsa. Ine mtumiki wanu ndinamuuza kuti, ‘Ndiikireni chishalo pabulu ndikwerepo kuti ndipite limodzi ndi mfumu,’ chifukwa ine mtumiki wanu ndine wolumala.+