2 Samueli 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma mtumiki wangayo anakuuzani inu mbuyanga mfumu+ zinthu zabodza zokhudza ine mtumiki wanu. Komabe inu mbuyanga muli ngati mngelo wa Mulungu woona, choncho chitani zilizonse zomwe mukuona kuti nʼzabwino.
27 Koma mtumiki wangayo anakuuzani inu mbuyanga mfumu+ zinthu zabodza zokhudza ine mtumiki wanu. Komabe inu mbuyanga muli ngati mngelo wa Mulungu woona, choncho chitani zilizonse zomwe mukuona kuti nʼzabwino.