2 Samueli 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Inu mbuyanga mfumu, mukanatha kupha anthu onse a mʼnyumba ya bambo anga. Koma munaika ine mtumiki wanu mʼgulu la anthu amene amadya patebulo lanu.+ Choncho ndilibe chifukwa chomveka kuti ndipitirize kudandaula kwa inu mfumu.”
28 Inu mbuyanga mfumu, mukanatha kupha anthu onse a mʼnyumba ya bambo anga. Koma munaika ine mtumiki wanu mʼgulu la anthu amene amadya patebulo lanu.+ Choncho ndilibe chifukwa chomveka kuti ndipitirize kudandaula kwa inu mfumu.”