2 Samueli 19:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Barizilai+ wa ku Giliyadi anabwera kudera la Yorodano kuchokera ku Rogelimu kuti adzaperekeze mfumu mpaka kuwoloka mtsinje wa Yorodano.
31 Ndiyeno Barizilai+ wa ku Giliyadi anabwera kudera la Yorodano kuchokera ku Rogelimu kuti adzaperekeze mfumu mpaka kuwoloka mtsinje wa Yorodano.