2 Samueli 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Barizilai anali ndi zaka 80 ndipo anali wokalamba kwambiri. Pamene Mfumu Davide anali ku Mahanaimu,+ Barizilai ankamupatsa chakudya popeza anali wolemera kwambiri. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:32 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2018, tsa. 9
32 Barizilai anali ndi zaka 80 ndipo anali wokalamba kwambiri. Pamene Mfumu Davide anali ku Mahanaimu,+ Barizilai ankamupatsa chakudya popeza anali wolemera kwambiri.