35 Panopa ndili ndi zaka 80.+ Kodi ndingasiyanitse chabwino ndi choipa? Kodi ine mtumiki wanu ndingamve kukoma kwa zakudya ndi zakumwa? Nanga ndingathenso kumvetsera nyimbo za amuna ndi akazi oimba?+ Ndiye ine mtumiki wanu ndikulemetseni chifukwa chiyani mbuyanga mfumu?