2 Samueli 19:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kenako anthu onse anayamba kuwoloka Yorodano, ndipo mfumu itawoloka, inakisa Barizilai+ nʼkumudalitsa. Zitatero, Barizilai anabwerera kwawo.
39 Kenako anthu onse anayamba kuwoloka Yorodano, ndipo mfumu itawoloka, inakisa Barizilai+ nʼkumudalitsa. Zitatero, Barizilai anabwerera kwawo.