2 Samueli 19:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Kenako anthu ena a ku Isiraeli anabwera kwa mfumu nʼkunena kuti: “Nʼchifukwa chiyani abale athu a ku Yuda akubweretsani mozemba inu mfumu, pamodzi ndi banja lanu komanso anthu onse amene munali nawo kutsidya la Yorodano?”+
41 Kenako anthu ena a ku Isiraeli anabwera kwa mfumu nʼkunena kuti: “Nʼchifukwa chiyani abale athu a ku Yuda akubweretsani mozemba inu mfumu, pamodzi ndi banja lanu komanso anthu onse amene munali nawo kutsidya la Yorodano?”+