2 Samueli 19:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Anthu a ku Yuda anayankha anthu a ku Isiraeli kuti: “Chifukwa chakuti mfumuyi ndi wachibale wathu.+ Ndiye inu mwakwiya nazo chifukwa chiyani? Kodi ife tadya zinthu zilizonse za mfumu kapena kulandira mphatso?”
42 Anthu a ku Yuda anayankha anthu a ku Isiraeli kuti: “Chifukwa chakuti mfumuyi ndi wachibale wathu.+ Ndiye inu mwakwiya nazo chifukwa chiyani? Kodi ife tadya zinthu zilizonse za mfumu kapena kulandira mphatso?”