-
2 Samueli 19:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Koma anthu a ku Isiraeli anayankha anthu a ku Yuda kuti: “Ifetu tili ndi mafuko 10 mu ufumu wa Davide, choncho tili ndi mphamvu zambiri kuposa inuyo. Ndiye nʼchifukwa chiyani mwatinyoza chonchi? Kodi ife sitinayenera kukhala patsogolo pobweretsa mfumu yathu?” Koma anthu a ku Isiraeliwo anagonja chifukwa cha zimene anthu a ku Yuda ananena.
-