-
2 Samueli 20:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno Yowabu anafunsa Amasa kuti: “Uli bwanji mʼbale wanga?” Kenako Yowabu anagwira ndevu za Amasa ndi dzanja lake lamanja ngati akufuna kumukisa.
-