2 Samueli 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atangomuchotsa pamsewupo, aliyense ankangodutsa kutsatira Yowabu pokasaka Sheba+ mwana wa Bikiri.