-
2 Samueli 20:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Yowabu ndi asilikali ake* anafika nʼkuzungulira mzinda wa Abele wa ku Beti-maaka womwe unazunguliridwa ndi malo okwera amene anthu amumzindawo anamanga. Yowabu ndi asilikali ake anamanganso malo okwera omenyerapo nkhondo. Anthu onse amene anali ndi Yowabu ankakumba pansi pa mpandawo kuti augwetse.
-