-
2 Samueli 20:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndiyeno mayi wina wanzeru wamumzindawo anafuula kuti: “Tamverani amuna inu, tamverani! Chonde tamuuzeni Yowabu abwere pafupipa kuti ndilankhule naye.”
-