2 Samueli 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine ndikuimira anthu okonda mtendere ndi okhulupirika a mu Isiraeli. Inu mukufuna kupha mzinda umene uli ngati mayi mu Isiraeli. Nʼchifukwa chiyani mukufuna kuwononga cholowa cha Yehova?”+
19 Ine ndikuimira anthu okonda mtendere ndi okhulupirika a mu Isiraeli. Inu mukufuna kupha mzinda umene uli ngati mayi mu Isiraeli. Nʼchifukwa chiyani mukufuna kuwononga cholowa cha Yehova?”+