2 Samueli 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adoramu+ ankatsogolera anthu olembedwa ntchito yokakamiza ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi ankalemba zimene zachitika.
24 Adoramu+ ankatsogolera anthu olembedwa ntchito yokakamiza ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi ankalemba zimene zachitika.