2 Samueli 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 mutipatse ana ake aamuna 7. Tipachika* mitembo yawo+ kuti Yehova aione.+ Tiipachika ku Gibeya, kwawo kwa Sauli, munthu amene Yehova anamusankha.”+ Ndiyeno mfumu inati: “Ndikupatsani.”
6 mutipatse ana ake aamuna 7. Tipachika* mitembo yawo+ kuti Yehova aione.+ Tiipachika ku Gibeya, kwawo kwa Sauli, munthu amene Yehova anamusankha.”+ Ndiyeno mfumu inati: “Ndikupatsani.”