2 Samueli 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma mfumu inamvera chisoni Mefiboseti+ mwana wamwamuna wa Yonatani, mwana wa Sauli, chifukwa cha lumbiro limene Davideyo ndi Yonatani+ mwana wa Sauli anapanga pamaso pa Yehova. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:7 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2022, tsa. 13
7 Koma mfumu inamvera chisoni Mefiboseti+ mwana wamwamuna wa Yonatani, mwana wa Sauli, chifukwa cha lumbiro limene Davideyo ndi Yonatani+ mwana wa Sauli anapanga pamaso pa Yehova.